Zamkatimu
October 2009
Magazini Yapadera
Mfundo Zothandiza Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino
Anthu amakonda kunena za zinthu zimene zimachititsa kuti banja lisamayende bwino koma osati zimene zimachititsa kuti banja liziyenda bwino. Nkhani zoyambirira za mu Galamukani! yapaderayi zikufotokoza mfundo 7 zimene zimachititsa kuti banja liziyenda bwino.
3 Mfundo 1: Muzikonda Kwambiri Banja Lanu
4 Mfundo 2: Khalani Wokhulupirika
5 Mfundo 3: Muzichita Zinthu Mogwirizana
9 Mfundo 7: Muzitsatira Malangizo Odalirika
14 Mabanja Amene Zinthu Zikuwayendera Bwino—Chigawo Choyamba
22 Mabanja Amene Zinthu Zikuwayendera Bwino—Chigawo Chachiwiri
Kodi Kutha kwa Banja—Kumakhudza Bwanji Ana? 18
Kodi n’chifukwa chiyani kutha kwa banja kumakhudza kwambiri ana okulirapo kusiyana ndi ana ang’onoang’ono?
Kodi ndinu kholo limene likulera lokha ana? Mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni.