Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 2/10 tsamba 15-31
  • Zoti Banja Likambirane

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zoti Banja Likambirane
  • Galamukani!—2010
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi pa Chithunzichi Pakusoweka Chiyani?
  • KODI MUKUDZIWA CHIYANI ZA MFUMU DAVIDE
  • ZITHUNZI ZOTI ANA APEZE
  • KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
  • MAYANKHO ALI PATSAMBA 31
  • Zoti Banja Likambirane
    Galamukani!—2010
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
Onani Zambiri
Galamukani!—2010
g 2/10 tsamba 15-31

Zoti Banja Likambirane

Kodi pa Chithunzichi Pakusoweka Chiyani?

Werengani Oweruza 7:15-22. Kenako yang’anani pa chithunzichi. Kodi n’chiyani chikusowekapo? Lembani mayankho anu m’mizere imene ili m’munsimu.

1. ․․․․․

2. ․․․․․

3. ․․․․․

KAMBIRANANI:

Kodi Gidiyoni ndi anyamata ake anapambana nkhondo chifukwa chiyani? N’chiyani chinalimbitsa mtima Gidiyoni ndi anyamata ake kuti akamenye nkhondo? Kodi inunso mungafunike kulimba mtima ngati Gidiyoni pa zinthu ziti?

KODI MUKUDZIWA CHIYANI ZA MFUMU DAVIDE

4. Kodi Davide anali ndi azikulu ake angati?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani 1 Samueli 16:10, 11.

․․․․․

5. Kodi mchimwene wake wa Davide woyamba kubadwa anali ndani?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani 1 Samueli 17:28.

․․․․․

KAMBIRANANI:

Kodi mukuganiza kuti n’chifukwa chiyani Davide ankachitiridwa nkhanza ndi mchimwene wake woyamba kubadwa? N’chifukwa chiyani si bwino kumuda mchimwene wanu kapena mlongo wanu?

ZITHUNZI ZOTI ANA APEZE

Pezani zithunzi izi m’magazini ino. Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowekapo.

TSAMBA 4 Kodi mwamuna ndi mkazi akakwatirana amakhala chiyani? Mateyo 19:․․․

TSAMBA 9 Kodi ndi “ulemerero” kuchita chiyani? Miyambo 19:․․․

TSAMBA 12 Kodi mtima ndi wotani? Yeremiya 17:․․․

TSAMBA 22 Kodi chikhulupiriro n’chiyani? Aheberi 11:․․․

● Mayankho ali patsamba 15

MAYANKHO ALI PATSAMBA 31

1. Lipenga.

2. Mbiya.

3. Miuni.

4. 7

5. Eliabu.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena