Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 10/09 tsamba 27-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2009
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Zinachitikira Kuti?
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • Kuchokera M’magazini Ino
  • Kodi Mukudziwa Chiyani Zokhudza Woweruza Gideoni?
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Zoti Banja Likambirane
    Galamukani!—2010
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
Onani Zambiri
Galamukani!—2009
g 10/09 tsamba 27-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Zinachitikira Kuti?

1. Kodi zomwe zasonyezedwa pachithunzipa zinachitikira mumzinda uti?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Machitidwe 18:1-3.

Lembani mzere wozungulira yankho lanu pamapu awa.

Roma

Korinto

Efeso

Tariso

◼ Kodi anthu atatuwa akutani?

․․․․․

◼ Kodi mwamuna ndi mkazi wakeyo maina awo ndani? Nanga mnzawoyo dzina lake ndani?

․․․․․

KAMBIRANANI:

Tchulani dzina la munthu winanso amene anathandizidwa ndi banjali?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Machitidwe 18:24-26.

Kodi mukuganiza kuti banjali linkakonda ntchito yotani, ndipo n’chifukwa chiyani mukuganiza choncho?

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungapeze zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

Kuchokera M’magazini Ino

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowapo.

TSAMBA 3 Kodi munthu amene sasamalira banja lake amakhala woipa kuposa ndani? 1 Timoteyo 5:․․․

TSAMBA 5 Kodi n’chifukwa chiyani awiri amaposa mmodzi? Mlaliki 4:․․․

TSAMBA 11 Kodi ndani amakhala ndi nzeru? Yobu 12:․․․

TSAMBA 29 Kodi tiyenera kupewa chiyani? 1 Atesalonika 4:․․․

Kodi Mukudziwa Chiyani Zokhudza Woweruza Gideoni?

Werengani Oweruza 6:1–7:25. Ndiyeno yankhani mafunso otsatirawa.

2. ․․․․․

Kodi anali wa fuko liti?

3. ․․․․․

Kodi anapulumutsa Aisiraeli ku mtundu uti?

4. ․․․․․

Zoona kapena zonama? Anakhala ndi moyo Mose asanabadwe.

KAMBIRANANI:

Kodi Gideoni anasonyeza khalidwe lotani atasankhidwa ndi Yehova?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Oweruza 6:14-16.

Kodi mukuganiza kuti khalidwe limeneli ndi lofunika? Fotokozani chifukwa chake mukuyankha choncho.

◼ Mayankho ali patsamba 27

MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31

1. Korinto.

◼ Akupanga hema.

◼ Akula ndi Purisikila, ndiponso Paulo.

2. Manase.—Oweruza 6:15.

3. Midiyani.—Oweruza 6:6.

4. Zonama.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena