Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 7/09 tsamba 11-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2009
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Zinachitikira Kuti?
  • Kuchokera M’magazini Ino
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • Kodi n’chiyani chimene mukudziwa chokhudza woweruza Otiniyeli?
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Zoti Banja Likambirane
    Galamukani!—2010
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
Onani Zambiri
Galamukani!—2009
g 7/09 tsamba 11-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Zinachitikira Kuti?

1. Kodi zinthu zotsatirazi zinachitikira mumzinda uti?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Machitidwe 2:1-13.

Pamapu awa lembani mzere wozungulira yankho lanu.

Atene

Yerusalemu

Babulo

◼ Kodi ophunzira ambiri a Yesu anali ochokera kuti?

․․․․․

◼ Kodi n’chifukwa chiyani anthu ena ankanyoza ophunzira a Yesu?

․․․․․

KAMBIRANANI:

Kodi nkhani imeneyi ikufanana ndiponso kusiyana bwanji ndi nkhani ya pa Genesis 11:1-9?

Kuchokera M’magazini Ino

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowa.

TSAMBA 4 Kodi n’chiyani chingameze munthu? 2 Akorinto 2:․․․

TSAMBA 6 Kodi mtendere wa Mulungu ungakuthandizeni bwanji? Afilipi 4:․․․

TSAMBA 28 Kodi ena amene ali ndi changu cha kwa Mulungu amasowa chiyani? Aroma 10:․․․

TSAMBA 29 Kodi tiyenera kumvera ndani? Machitidwe 5:․․․

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

Kodi n’chiyani chimene mukudziwa chokhudza woweruza Otiniyeli?

Werengani Oweruza 3:7-11. Ndiyeno yankhani mafunso otsatirawa.

2. ․․․․․

Kodi anali wa fuko lanji?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Yoswa 15:17, 20.

3. ․․․․․

Kodi iye anapulumutsa Aisiraeli kwa wolamulira uti?

4. ․․․․․

Zoona kapena zonama? Iye anakhala ndi moyo Mose asanabadwe.

KAMBIRANANI:

Kodi Kalebe yemwe anali malume ake a Otiniyeli anasonyeza chitsanzo chabwino chotani?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Numeri 14:6-9. Tchulani dzina la wachibale wanu aliyense amene mumamusirira, ndipo fotokozani chifukwa chake.

◼ Mayankho ali pa tsamba 11

MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31

1. Yerusalemu.—Machitidwe 2:5.

◼ Galileya.—Machitidwe 2:7.

◼ Ankaganiza kuti aledzera.—Machitidwe 2:13.

2. Yuda.—Yoswa 15:17, 20.

3. Kusani-Risataimu—Oweruza 3:8.

4. Zonama.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena