Zamkatimu
March 2010
M’chilengedwe Zinalipo Kale M’chilengedwe
Kodi tikuphunzira chiyani pa zimene anthu atulukira ndi zimene zinalipo kale m’chilengedwe?
10 Chilengedwe Chimatiphunzitsa Zambiri
16 Zilumba za Faeroe Zinalumikizana Mochititsa Chidwi
22 Anthu Akhala Akulambira Njoka kwa Zaka Zambiri
24 Manda a Pansi pa Nthaka a ku Odessa Ndi Ochititsa Chidwi
26 Chakudya Chomwe Tizilombo Timakonda
32 Yesu Anapereka Moyo Wake Kuti Awombole Anthu Ambiri
Ndinakopeka ndi Mboni za Yehova 12
Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chimene chinachititsa mkulu wa asilikali kukopeka ndi Mboni za Yehova.
Kodi Mbali Zonse za Baibulo N’zothandiza Masiku Ano? 28
Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene mfundo za m’Chilamulo cha Mose komanso nkhani yonena za mibadwo ya anthu imene ili m’Baibulo imakukhudzirani.