Zamkatimu
May 2010
Kodi Munthu Angatani Kuti Asiye Kusuta?
Ngati mumasuta fodya, kodi mungatani kuti musiye? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene mungathetsere chizolowezi choipa komanso chowonongetsa ndalama chimenechi.
6 Konzekerani Kukumana ndi Mavuto
10 Kuyenda pa Bwato Ndi Njira Yabwino Yoyendera ku Canada
12 Kodi Mungatani Kuti Muchepetse Vuto Lochita Chibwibwi?
15 Anthu a ku Thailand Amavala Mogometsa
20 Anakwanitsa Kuchita Zinthu Zimene Zinali Zosatheka
29 Kugunda kwa Mtima Kumagwirizana ndi Kutalika kwa Moyo
32 Kodi Mungatani Kuti Muyandikire Mulungu?
Kodi Ndizitani Kuti Ndizigwiritsa Ntchito Ndalama Mwanzeru? 18
M’nthawi ino ya mavuto a zachuma, ndi bwino kupeza malangizo amene angakuthandizeni kuti muziona ndalama moyenerera komanso kugwiritsa ntchito ndalama mwanzeru.
Ngakhale Kuti Ndinalumala, Ndine Wosangalalabe 24
José anakomoka kwa miyezi itatu ndipo atatsitsimuka anazindikira kuti manja ndi miyendo yake sizikugwiranso ntchito. Werengani nkhaniyi kuti mumve zimene zinamuthandiza kuti akhalebe wosangalala ngakhale kuti anakumana ndi vutoli.