Zamkatimu
September 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
Baibulo likhoza kukuthandizani kupeza mayankho a mafunso ambiri amene achinyamata amadzifunsa. Ena mwa mafunsowa ndi akuti:
• “Kodi Ndizitani Ngati Ena Akundichitira Zachipongwe?”
• “Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Mameseji a Pafoni?”
• “Kodi Ndingatani Ngati Ndikudwala Matenda Enaake Aakulu?”
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandizira ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)