Zamkatimu
December 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Ofalitsa Nkhani Tingawakhulupirire?
TSAMBA 4 MPAKA 7
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
Mukhoza kupeza mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene achinyamata amadzifunsa. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndingatani Ngati Anthu Ena Akukonda Kunena za Ine?”
• “Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani pa Nkhani Yotumizirana Mameseji ndi Zinthu Zina Zolaula?”
Werengani nkhanizi kuti mudziwe mmene Baibulo lingathandizire achinyamata kuthana ndi mavuto amene amakumana nawo.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA >ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)