Zamkatimu
June 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mungatani Kuti Mukhale Bwenzi Labwino?
TSAMBA 4 MPAKA 7
12 Zimene Mungachite Kuti Mupewe Chiseyeye
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU YA
ACHINYAMATA
Mungapeze mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene achinyamata amadzifunsa. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndingakwanitse Kukakhala Pandekha?”
• “Kodi Ndingatani Kuti Ndisamangoganizira Zogonana?”
Mungathenso kuonera vidiyo yachingelezi yakuti, “What Your Peers Say—Cell Phones” pa webusaiti yathu ya www.pr418.com/en
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)