Zamkatimu
March 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mukudziwa Mmene Mulungu Analengera Zinthu Zonsezi?
TSAMBA 4 MPAKA 7
12 Misozi Yathu Ndi Yodabwitsa Kwambiri
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
Mungapeze mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene achinyamata amakhala nawo. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndingatani Ngati Palibe Munthu Amene Ndingacheze Naye Momasuka?”
• “Kodi Ndingatani Kuti Ndisamachite Zinthu Mozengereza?”
• “Kodi Munthu Ameneyu Ndi Woyenera Kuti Ndimange Naye Banja?”
(Fufuzani pa mawu akuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)