Zamkatimu
July 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mungatani Mutakumana Ndi Vuto Lalikulu?
Katundu Wanu Yense Atawonongeka
Atakupezani Ndi Matenda Aakulu
Munthu wa M’banja Lanu Akamwalira
TSAMBA 4 MPAKA 7
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU YA
ACHINYAMATA
Mungapeze mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene achinyamata amadzifunsa. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndingatani Ngati Anthu Ena Akukonda Kunena za Ine?”
• “Kodi Ndingatani Kuti Ndisamachite Zinthu Mozengereza?”
Mungathenso kuonera vidiyo yachingelezi yakuti, What Your Peers Say—Money pa webusaiti yathu ya www.jw.org/en.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)