Zamkatimu
April 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Kudzipha Ndi Njira Yabwino Yothetsera
2 Pali Zimene Zingakuthandizeni
3 Pali Chiyembekezo Choti Zinthu Zidzakhala Bwino M’tsogolo
TSAMBA 6 MPAKA 9
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
Mungapeze mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene achinyamata amakhala nawo. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani pa Nkhani Yotumizirana Mameseji ndi Zinthu Zina Zolaula?”
• “Kodi Ndingatani Ngati Ndilibe Mnzanga?”
• “Kodi Ndingatani Anthu Ena Akamandivutitsa?”
(Fufuzani pa mawu akuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)