Zamkatimu
May 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mungatani Ngati Mukuvutika Maganizo?
TSAMBA 4 MPAKA 7
12 Ntchito Yofufuza Anthu Amene Ankawaganizira Kuti Ndi Mfiti ku Ulaya
16 ‘Nzeru Ikufuula’—Kodi Inuyo Mukuimva?
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU YA
ACHINYAMATA
Mungapeze mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene achinyamata amadzifunsa. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndine Munthu Wodalirika?”
• “Kodi Ndafika Poti N’kukhala ndi Chibwenzi?”
• “Kodi Ndingachite Chiyani Ngati Makolo Anga Akufuna Kuthetsa Banja Lawo?”
Mungathenso kuonera vidiyo yachingelezi yakuti, “What Your Peers Say—Body Image” pa webusaiti yathu ya jw.org/en.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)