Zamkatimu
August 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
10 Amaphunzitsa Baibulo Komanso Kuwerenga ndi Kulemba
14 Sanasiye Kutsatira Zimene Amakhulupirira
MUNGAPEZENSO ZINTHU ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU
ACHINYAMATA
Kodi mungatani kuti mukhale ndi moyo wathanzi? Onerani vidiyo yachingelezi ya mutu wakuti Healthy Lifestyles.
Mukhoza kupeza mayankho a mafunso amene mungafunsidwe kusukulu monga akuti: “Kodi Zinthu Zinachita Kulengedwa?”
(Pitani pomwe alemba kuti BIBLE TEACHINGS > TEENAGERS)
ANA
Onerani vidiyo yophunzitsa ana makhalidwe abwino monga yakuti Muzimvera Makolo Anu.
(Pitani pomwe alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)