Zamkatimu
September 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MUNGAPEZENSO ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU
ACHINYAMATA
Onerani vidiyo yachingelezi yomwe ikufotokoza zimene achinyamata amanena pa nkhani ya ndalama.
(Pitani pa webusaiti yachingelezi pamene palembedwa kuti BIBLE TEACHINGS > TEENAGERS)
ANA
Onerani vidiyo yachingelezi. Ana awiri apatsidwa zoseweretsa ndi makolo awo.
Kodi aziseweretsera limodzi zimene makolo awo awapatsazo?
(Pitani pa webusaiti yachingelezi pamene palembedwa kuti BIBLE TEACHINGS > CHILDREN)