Zamkatimu
December 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Kodi N’zotheka Kukhala Ndi Banja Losangalala?
Kodi n’chiyani chimachititsa kuti anthu azikangana m’banja?
10 Kodi Munazionapo Nsomba Zikuluzikulu Izi?
15 Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2015
MUNGAPEZENSO ZINTHU ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU
MAVIDIYO
Onerani vidiyo yachingeleziyi kuti muone mmene Kalebe ndi Sofiya akusangalalira chifukwa chopereka mphatso.
(Pitani pomwe palembedwa kuti, BIBLE TEACHINGS > CHILDREN)
A James Ryan anabadwa ndi vuto losamva ndipo kenako anasiya kuona. Onerani vidiyo yachingeleziyi kuti muone mmene banja lawo komanso anzawo awathandizira kuti azikhala moyo wosangalala.
(Pitani pomwe palembedwa kuti, ZOKHUDZA IFEYO > ZIMENE TIMACHITA)