Zamkatimu
May 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
10 “Mulungu Akutithandiza Kuti Tiiwale Zakale”
MUNGAPEZENSO ZINTHU ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU
ZOKHUDZA IFEYO
Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?
Vidiyoyi ingakuthandizeni kudziwa zomwe zimachitika pa Nyumba ya Ufumu ya Mboni za Yehova padziko lonse. Ingakuthandizeninso kudziwa anthu amene angafike pa Nyumba ya Ufumu.
(Pitani pomwe alemba kuti, ZOKHUDZA IFEYO > MISONKHANO)
ANA
Onerani vidiyo ya ana yachingeleziyi, yomwe ikusonyeza kuti Kalebe amakhala wosangalala kwambiri akasonyeza makhalidwe abwino.
(Pitani pomwe alemba kuti, BIBLE TEACHINGS > CHILDREN)