Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g18 No. 3 tsamba 16
  • Mfundo Zothandiza Amene Aferedwa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mfundo Zothandiza Amene Aferedwa
  • Galamukani!—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
    Galamukani!—2018
  • “Kodi Ndingakhale Bwanji ndi Chisoni Changa?”
    Galamukani!—1988
  • Mawu Oyamba
    Galamukani!—2018
  • Kodi Ndingakhale Motani ndi Chisoni Changa?
    Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira
Onani Zambiri
Galamukani!—2018
g18 No. 3 tsamba 16
Bambo woferedwa akulimbikitsidwa chifukwa chowerenga magaziniyi

MFUNDO ZOTHANDIZA AMENE AFEREDWA

Nkhani za M’magaziniyi Mfundo Zothandiza Amene Aferedwa

  • KUVUTIKA MAGANIZO CHIFUKWA CHOFEREDWA

    Kodi munthu akaferedwa amakumana ndi mavuto otani? N’chifukwa chiyani anthu amene aferedwa amafunika kuwalimbikitsa?

  • MAVUTO AMENE MUNGAKUMANE NAWO

    Nkhaniyi ikufotokoza maganizo olakwika omwe anthu ena amakhala nawo komanso zimene zinachitikirapo ena ataferedwa. Ngati inunso muli ndi chisoni chifukwa choferedwa, nkhaniyi ingakuthandizeni kudziwa zimene anthu ambiri omwe anaferedwa amakumana nazo.

  • ZIMENE ZINGAKUTHANDIZENI MUKAFEREDWA​—ZIMENE MUNGACHITE PANOPA

    Kodi mungatsatire njira ziti kuti musamavutike kwambiri ndi chisoni? Nkhaniyi ikufotokoza njira zingapo zomwe zathandizapo anthu ena. Njirazi zili ndi mfundo zochokera m’Baibulo.

  • MFUNDO ZOFUNIKA KWAMBIRI KWA ANTHU OMWE AFEREDWA

    Werengani nkhaniyi kuti mudziwe njira zomwe ena atsatira pa nthawi yovutayi ndipo muone mmene inunso zingakuthandizireni.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena