Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g19 No. 2 tsamba 16
  • Mfundo Zina Zothandiza Makolo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mfundo Zina Zothandiza Makolo
  • Galamukani!—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Mungapeze Thandizo
    Galamukani!—2020
  • Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?
    Kodi Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo Tingawapeze Kuti?
  • Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Bwanji?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Bwanji?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Yambani Kuphunzira Baibulo
Onani Zambiri
Galamukani!—2019
g19 No. 2 tsamba 16

MFUNDO ZINA ZOTHANDIZA MAKOLO

Mzimayi akuwerenga Baibulo

Monga mwaonera, malangizo amene ali m’magaziniyi ndi ochokera m’Baibulo. M’Baibulo mumapezeka malangizo abwino kwambiri amene angathandize kuti banja likhale losangalala. Mfundo zake zimathandiza munthu kukhala woganiza bwino komanso kuti azisankha zinthu mwanzeru.​—Miyambo 1:1-4.

BAIBULO LIMAYANKHANSO MAFUNSO OFUNIKA KWAMBIRI MONGA AKUTI:

  • Kodi cholinga cha moyo n’chiyani?

  • Kodi Mulungu ndi amene amachititsa kuti tizivutika?

  • Kodi chimachitika n’chiyani munthu akamwalira?

Tikukulimbikitsani kuti mufufuze m’Baibulo mayankho a mafunso amenewa komanso ena. Onerani kavidiyo kakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? popanga sikani kachidindo aka kapena pitani pa www.pr418.com.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena