Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g20 No. 1 tsamba 16
  • “Mtima Wodekha Ndiwo Moyo wa Munthu”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Mtima Wodekha Ndiwo Moyo wa Munthu”
  • Galamukani!—2020
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • ANTHU A PABANJA
  • MAKOLO
  • ACHINYAMATA
  • Kodi mukufuna kudziwa zambiri?
    Galamukani!—2021
  • Achinyamata Ambiri Akuvutika Ndi Matenda Amaganizo—Kodi Baibulo Limanena Zotani?
    Nkhani Zina
  • Phunzitsani Ana Anu Kuti Azigwiritsa Ntchito Intaneti Moyenera
    Galamukani!—2014
  • Kulemekezana M’banja
    Galamukani!—2024
Onani Zambiri
Galamukani!—2020
g20 No. 1 tsamba 16

“Mtima Wodekha Ndiwo Moyo Wa Munthu”

Mwamuna ndi mkazi wake akuwerenga patabuleti yawo.

Mawu amenewa omwe amapezeka pa Miyambo 14:30, analembedwa pafupifupi zaka 3,000 zapitazo. Mawuwa amasonyeza kuti mfundo za m’Baibulo n’zothandiza nthawi zonse. Ngati mukufuna kudziwa zambiri, pitani pawebusaiti yathu ya jw.org. Pawebusaitiyi mungapezepo mavidiyo, makatuni, zochitika pamoyo wa anthu ena komanso nkhani zambiri zomwe zingakuthandizeni kuchepetsa nkhawa. Mungapezepo nkhani zokhudza:

ANTHU A PABANJA

  • Kuthetsa Mikangano

  • Zimene Mungachite Kuti Muzigwirizana ndi Achibale

  • Mungatani Kuti Musamasunge Chakukhosi?

MAKOLO

  • Zimene Mungachite Kuti Muzimasukirana ndi Mwana Wanu

  • Ngati Mwana Wanu Wamkazi Akuvutika Maganizo

  • Phunzitsani Ana Anu Kuti Azigwiritsa Ntchito Intaneti Moyenera

ACHINYAMATA

  • Kodi Mungatani Kuti Anzanu Asiye Kukuvutitsani?

  • Kodi Ndingatani Kuti Ndizigona Mokwanira?

  • N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kukhala Mwamtendere ndi Abale Anga?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena