Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 117
  • Tiziphunzitsidwa Ndi Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tiziphunzitsidwa Ndi Yehova
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Tiziphunzitsidwa
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Yendani ndi Mulungu!
    Imbirani Yehova
  • Muziyenda Ndi Mulungu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nyimbo Yatsopano
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 117

Nyimbo 117

Tiziphunzitsidwa Ndi Yehova

Losindikizidwa

(Yesaya 50:4; 54:13)

1. Bwerani mosangalala muphunzire.

“Bwerani m’dzamwe madzi a moyo.”

Dzadyeni inu nonse anjala,

Dzalandirenitu malangizo.

2. Tisaleketu kusonkhana pamodzi,

Tiziphunzitsidwa ndi Mulungu.

Kuno n’kumene kuli abale,

Kuno n’kumene kulitu mzimu.

3. Lilime lophunzitsidwa choonadi

Limabweretsa chisangalalo.

Tipezeke ndi anthu a M’lungu,

Tizipezeka pamisonkhano.

(Onaninso Aheb. 10:24, 25; Chiv. 22:17.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena