Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 55
  • Musawaope

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Musawaope
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Musawaope!
    Imbirani Yehova
  • Musawaope!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • “Mawonekedwe a Dziko Lino Akusintha”
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Moyo Wopanda Mapeto—Potsiriza!
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 55

NYIMBO 55

Musawaope

Losindikizidwa

(Mateyu 10:28)

  1. 1. Pitanibe anthu anga

    Lengezani Ufumu.

    Musaope mdaniyo.

    Dziwitsani achidwi

    Kuti Mwana wanga Yesu

    Wamugwetsa mdaniyo.

    Posachedwa adzam’manga

    Sadzazuzanso anthu.

    (KOLASI)

    Musaope anthu anga.

    Olo muwopsezedwe

    Ndidzakutetezerani

    Monga mwana wa diso.

  2. 2. Adani angachuluke

    Ndi kukuopsezani,

    N’kukunyengererani

    Kuti mupusitsidwe,

    Musaope anthu anga.

    Kaya akuzunzeni,

    Ndidzakutetezerani

    Mpaka onse atatha.

    (KOLASI)

    Musaope anthu anga.

    Olo muwopsezedwe

    Ndidzakutetezerani

    Monga mwana wa diso.

  3. 3. Sindingakuiwaleni

    Ndidzakutetezani.

    Ngakhale akupheni

    Ndidzagonjetsa imfa.

    Musaope opha thupi

    Sangawononge moyo.

    Choncho khulupirikani

    Mudzalandira moyo.

    (KOLASI)

    Musaope anthu anga.

    Olo muwopsezedwe

    Ndidzakutetezerani

    Monga mwana wa diso.

(Onaninso Deut. 32:10; Neh. 4:14; Sal. 59:1; 83:​2, 3.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena