Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • syr19 tsamba 2
  • Ziwerengero Zonse za 2019

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ziwerengero Zonse za 2019
  • Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2019 la Mboni za Yehova Padziko Lonse.
  • Nkhani Yofanana
  • Ziwerengero Zonse za 2020
    Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2020 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziwerengero Zonse za 2018
    Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2018 la Mboni za Yehova
  • Ziwerengero Zonse za 2021
    Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2021 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziwerengero Zonse za 2017
    Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2017 la Mboni za Yehova
Onani Zambiri
Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2019 la Mboni za Yehova Padziko Lonse.
syr19 tsamba 2

Ziwerengero Zonse za 2019

  • Nthambi za Mboni za Yehova: 87

  • Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 240

  • Mipingo Yonse: 119,712

  • Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 20,919,041

  • Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 20,526

  • Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikiraa: 8,683,117

  • Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 8,471,008

  • Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kuchokera mu 2018: 1.3

  • Obatizidwa Onseb: 303,866

  • Avereji ya Apainiyac Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,277,738

  • Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 464,980

  • Maola Onse Amene Tinalalikira: 2,088,560,437

  • Avereji ya Maphunziro a Baibulod Mwezi Uliwonse: 9,618,182

M’chaka cha utumiki cha 2019,e a Mboni za Yehova anagwiritsa ntchito ndalama zoposa madola $224 miliyoni posamalira apainiya apadera, amishonale ndi oyang’anira dera pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale ndi alongo okwana 20,858 amene akutumikira m’maofesi a nthambi. Onsewa ali m’Gulu Lapadziko Lonse la Atumiki Apadera a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.

a Wofalitsa ndi munthu amene amalalikira mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengerochi, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?”

b Kuti mudziwe zimene mungachite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?”

c Mpainiya ndi wa Mboni wachitsanzo chabwino amene amadzipereka kuti azilalikira uthenga wabwino kwa maola enaake mwezi uliwonse.

d Kuti mudziwe zambiri, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Phunziro la Baibulo N’chiyani?”

e Chaka chautumiki cha 2019 chinayamba pa 1 September 2018, ndipo chinatha pa 31 August 2019.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena