Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • CO-pgm20 tsamba 6-7
  • Lamlungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Lamlungu
  • Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2020
  • Nkhani Yofanana
  • Lamlungu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024
  • Lamlungu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2017
  • Lamlungu
    Pulogalamu ya Msonkhano wa 2025
  • Lamlungu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2023
Onani Zambiri
Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2020
CO-pgm20 tsamba 6-7

LAMLUNGU

“Sangalala mwa Yehova, ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako”​—Salimo 37:4

M’MAWA

  • 9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 9:30 Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero

  • 9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Tikhoza Kumasangalalabe Ngakhale Kuti . . .

    • • Tikukumana ndi Masautso (Aroma 5:3-5; 8:35, 37)

    • • Tikukumana ndi Zowawa (2 Akorinto 4:8; 7:5)

    • • Tikuzunzidwa (Mateyu 5:11, 12)

    • • Tikuvutika ndi Njala (Afilipi 4:11-13)

    • • Tikuvutika ndi Usiwa (1 Akorinto 4:11, 16)

    • • Tikukumana ndi Zoopsa (2 Akorinto 1:8-11)

    • • Tikuopsezedwa ndi Lupanga (2 Timoteyo 4:6-8)

  • 11:10 Nyimbo Na. 9 ndi Zilengezo

  • 11:20 NKHANI YA ONSE: Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi Chuma Chomwe Sichiwonjezerapo Ululu? (Miyambo 10:22; 1 Timoteyo 6:9, 10; Chivumbulutso 21:3-5)

  • 11:50 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 12:20 Nyimbo Na. 84 ndi Kupuma

MASANA

  • 1:40 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 1:50 Nyimbo Na. 62

  • 1:55 VIDIYO: Nehemiya: “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”​—Mbali Yachiwiri (Nehemiya 8:1–13:30; Malaki 1:6–3:18)

  • 2:40 Nyimbo Na. 71 ndi Zilengezo

  • 2:50 ‘Muzisangalala Kwambiri mwa Yehova’ (Salimo 16:8, 9, 11; 37:4)

  • 3:50 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena