Lamlungu
“Adzalambira Atate motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi”—Yohane 4:23
M’mawa
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 140 Komanso Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Zimene Tikuphunzira pa Zomwe Yesu Ananena
• “Kubadwa mwa Madzi ndi Mzimu” (Yohane 3:3, 5)
• “Palibe Munthu Amene Anakwera Kumwamba” (Yohane 3:13)
• ‘Fikani Pamene Pali Kuwala’ (Yohane 3:19-21)
• “Munthu Ameneyo Ndi Ineyo” (Yohane 4:25, 26)
• “Chakudya Changa” (Yohane 4:34)
• “M’mindamo . . . Mwayera Kale Ndipo M’mofunika Kukolola” (Yohane 4:35)
11:05 Nyimbo Na. 37 Komanso Zilengezo
11:15 NKHANI YA ONSE: Kodi Zomwe Mumakhulupirira Ndi Zoona? (Yohane 4:20-24)
11:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
12:15 Nyimbo Na. 84 Komanso Kupuma
Masana
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 77
1:50 VIDIYO:
Uthenga Wabwino wa Yesu: Gawo 3
“Munthu Ameneyo Ndi Ineyo” (Yohane 3:1–4:54; Mateyu 4:12-20; Maliko 1:19, 20; Luka 4:16–5:11)
2:35 Nyimbo Na. 20 Komanso Zilengezo
2:45 Kodi Mwaphunzira Chiyani?
2:55 Pitirizani Kukhala M’kachisi Wamkulu Wauzimu wa Yehova (Aheberi 10:21-25; 13:15, 16; 1 Petulo 1:14-16; 2:21)
3:45 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza