Lamlungu
“Ngati mutakhala ndi chikhulupiriro . . . , zidzachitikadi”—Mateyu 21:21
M’MAWA
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Tsanzirani Akazi a Chikhulupiriro Cholimba
• Sara (Aheberi 11:11, 12)
• Rahabi (Aheberi 11:31)
• Hana (1 Samueli 1:10, 11)
• Mtsikana wa Chiisiraeli Yemwe Anali Kapolo (2 Mafumu 5:1-3)
• Maria Mayi Ake a Yesu (Luka 1:28-33, 38)
• Mayi wa ku Foinike (Mateyu 15:28)
• Marita (Yohane 11:21-24)
• Zitsanzo za Akazi a Masiku Ano (Salimo 37:25; 119:97, 98)
11:05 Nyimbo Na. 142 ndi Zilengezo
11:15 NKHANI YA ONSE: “Muzikhulupirira Uthenga Wabwino” (Maliko 1:14, 15; Mateyu 9:35; Luka 8:1)
11:45 Nyimbo Na. 22 ndi Kupuma
MASANA
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 126
1:50 VIDIYO: Danieli Anali Munthu Wachikhulupiriro Cholimba— Mbali Yachiwiri (Danieli 5:1–6:28; 10:1–12:13)
2:40 Nyimbo Na. 150 ndi Zilengezo
2:45 Khalani Olimba Chifukwa cha Chikhulupiriro Chanu (Danieli 10:18, 19; Aroma 4:18-21)
3:45 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza