Loweruka
“Kudzipereka kwanga panyumba yanu kudzakhala ngati moto umene ukuyaka mumtima mwanga”—Yohane 2:17
M’mawa
8:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 93 Komanso Pemphero
8:40 “Kodi Mukufunafuna Chiyani?” (Yohane 1:38)
8:50 VIDIYO:
Uthenga Wabwino wa Yesu: Gawo 2
“Uyu ndi Mwana Wanga”—Mbali Yachiwiri (Yohane 1:19–2:25)
9:20 Nyimbo Na. 54 Komanso Zilengezo
9:30 NKHANI YOSIYIRANA: Muzitsanzira Anthu Amene Ankakonda Kulambira Koyera
• Yohane M’batizi (Mateyu 11:7-10)
• Andireya (Yohane 1:35-42)
• Petulo (Luka 5:4-11)
• Yohane (Mateyu 20:20, 21)
• Yakobo (Maliko 3:17)
• Filipo (Yohane 1:43)
• Natanayeli (Yohane 1:45-47)
10:35 NKHANI YA UBATIZO: N’chifukwa Chiyani Mukubatizidwa? (Malaki 3:17; Machitidwe 19:4; 1 Akorinto 10:1, 2)
11:05 Nyimbo Na. 52 Komanso Kupuma
Masana
12:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 36
12:50 NKHANI YOSIYIRANA: Mmene Tingagwiritsire Ntchito Zomwe Tikuphunzira pa Chozizwitsa Choyambirira cha Yesu
• Kusonyeza Chifundo (Agalatiya 6:10; 1 Yohane 3:17)
• Kukhala Odzichepetsa (Mateyu 6:2-4; 1 Petulo 5:5)
• Kukhala Opatsa (Deuteronomo 15:7, 8; Luka 6:38)
1:20 Kodi “Mwanawankhosa wa Mulungu” Akuchotsa Bwanji Uchimo? (Yohane 1:29; 3:14-16)
1:45 NKHANI YOSIYIRANA: Kukwaniritsidwa kwa Maulosi Onena za Mesiya—Mbali Yachiwiri
• Anadzipereka Kwambiri pa Nyumba ya Yehova (Salimo 69:9; Yohane 2:13-17)
• Analengeza “Uthenga Wabwino kwa Anthu Ofatsa” (Yesaya 61:1, 2)
• Anaonetsa “Kuwala Kwakukulu” ku Galileya (Yesaya 9:1, 2)
2:20 Nyimbo Na. 117 Komanso Zilengezo
2:30 “Chotsani Izi Muno” (Yohane 2:13-16)
3:00 “Ine Ndidzamumanga” (Yohane 2:18-22)
3:35 Nyimbo Na. 75 Komanso Pemphero Lomaliza