Lachisanu
“Yehova Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira”—Mateyu 4:10
M’mawa
8:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 74 Komanso Pemphero
8:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: Kodi Kulambira Koyera Kumatanthauza Chiyani? (Yesaya 48:17; Malaki 3:16)
9:10 VIDIYO:
Uthenga Wabwino wa Yesu: Gawo 2
“Uyu ndi Mwana Wanga”—Mbali Yoyamba (Mateyu 3:1–4:11; Maliko 1:12, 13; Luka 3:1–4:7; Yohane 1:7, 8)
9:40 Nyimbo Na. 122 Komanso Zilengezo
9:50 NKHANI YOSIYIRANA: Kukwaniritsidwa kwa Maulosi Onena za Mesiya—Mbali Yoyamba
• Anavomerezedwa ndi Mulungu (Salimo 2:7; Mateyu 3:16, 17; Machitidwe 13:33, 34)
• Anabadwira Mumzere wa Mfumu Davide (2 Samueli 7:12, 13; Mateyu 1:1, 2, 6)
• Anadzozedwa Kukhala “Mesiya Mtsogoleri” (Danieli 9:25; Luka 3:1, 2, 21-23)
10:45 Ndi Ndani Kwenikweni Amene Akulamulira Dzikoli? (Maliko 12:17; Luka 4:5-8; Yohane 18:36)
11:15 Nyimbo Na. 22 Komanso Kupuma
Masana
12:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 121
12:50 NKHANI YOSIYIRANA: Tsanzirani Zimene Yesu Anayankha Pamene Satana Ankamuyesa
• Muzichita Zimene Mawu a Yehova Amanena (Mateyu 4:1-4)
• Musamamuyese Yehova (Mateyu 4:5-7)
• Muzilambira Yehova Yekha (Mateyu 4:10; Luka 4:5-7)
• Muziikira Kumbuyo Choonadi (1 Petulo 3:15)
1:50 Nyimbo Na. 97 Komanso Zilengezo
2:00 NKHANI YOSIYIRANA: Zomwe Tikuphunzira pa Moyo wa M’nthawi ya Yesu
• Chipululu cha Yudeya (Mateyu 3:1-4; Luka 4:1)
• Chigwa cha Yorodano (Mateyu 3:13-15; Yohane 1:27, 30)
• Yerusalemu (Mateyu 23:37, 38)
• Samariya (Yohane 4:7-9, 40-42)
• Galileya (Mateyu 13:54-57)
• Foinike (Luka 4:25, 26)
• Siriya (Luka 4:27)
3:10 Kodi Yesu Amaona Chiyani mwa Inu? (Yohane 2:25)
3:45 Nyimbo Na. 34 Komanso Pemphero Lomaliza