Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • CO-pgm22 tsamba 2-3
  • Lachisanu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Lachisanu
  • Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2022
  • Nkhani Yofanana
  • Loweruka
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2022
  • Lachisanu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2019
  • Lamlungu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2022
  • Lamlungu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024
Onani Zambiri
Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2022
CO-pgm22 tsamba 2-3
Malo a mtundu wa buluu komanso wa girini.

Lachisanu

“Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendere”​—Salimo 29:11

M’Mawa

  • 9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 9:30 Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero

  • 9:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: Yehova Ndi “Mulungu Amene Amapatsa Mtendere” (Aroma 15:33; Afilipi 4:6, 7)

  • 10:10 NKHANI YOSIYIRANA: Chikondi Chimatithandiza Kukhala ndi Mtendere Weniweni

    • • Kukonda Mulungu (Mateyu 22:37, 38; Aroma 12:17-19)

    • • Kukonda Anzathu (Mateyu 22:39; Aroma 13:8-10)

    • • Kukonda Mawu a Mulungu (Salimo 119:165, 167, 168)

  • 11:05 Nyimbo Na. 24 ndi Zilengezo

  • 11:15 KUWERENGA BAIBULO MWASEWERO: Yakobo Anali Munthu Wokonda Mtendere (Genesis 25:21–33:11)

  • 11:45 “Ntchito ya Chilungamo Chenicheni Idzakhala Mtendere” (Yesaya 32:17; 60:21, 22)

  • 12:15 Nyimbo Na. 97 ndi Kupuma

Masana

  • 1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 1:45 Nyimbo Na. 144

  • 1:50 NKHANI YOSIYIRANA: Tizisangalala ndi Malonjezo a Mulungu Okhudza Mtendere

    • • “Atumiki Anga Adzadya . . . Atumiki Anga Adzamwa” (Yesaya 65:13, 14)

    • • “Iwo Adzamanga Nyumba . . . Adzabzala Minda ya Mpesa” (Yesaya 65:21-23)

    • • “Mmbulu ndi Mwana wa Nkhosa Zidzadyera Pamodzi” (Yesaya 11:6-9; 65:25)

    • • “Palibe . . . Amene Adzanene Kuti: ‘Ndikudwala.’” (Yesaya 33:24; 35:5, 6)

    • • “Iye Adzameza Imfa Kwamuyaya” (Yesaya 25:7, 8)

  • 2:50 Nyimbo Na. 35 ndi Zilengezo

  • 3:00 NKHANI YOSIYIRANA: Zimene Zingathandize Kuti M’banja Muzikhala Mtendere

    • • Muzikondana Komanso Kulemekezana (Aroma 12:10)

    • • Muzilankhulana Nthawi Zonse (Aefeso 5:15, 16)

    • • Muzichita Zinthu Mogwirizana (Mateyu 19:6)

    • • Muzilambira Yehova Limodzi (Yoswa 24:15)

  • 3:55 Muzithandiza “Kalonga Wamtendere” Mokhulupirika (Yesaya 9:6, 7; Tito 3:1, 2)

  • 4:15 Tisamapusitsidwe ndi Mtendere Wosakhalitsa (Mateyu 4:1-11; Yohane 14:27; 1 Atesalonika 5:2, 3)

  • 4:50 Nyimbo Na. 112 ndi Pemphero Lomaliza

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena