Loweruka
“Adzakupezeni opanda banga, opanda chilema ndiponso muli mu mtendere”—2 Petulo 3:14
M’Mawa
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 58 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Muzikhala Okonzeka Kulalikira “Uthenga Wabwino Wamtendere”
• Pitirizani Kuchita Khama (Aroma 1:14, 15)
• Muzikonzekera Mokwanira (2 Timoteyo 2:15)
• Muziyamba Ndinu Kuwalankhula (Yohane 4:6, 7, 9, 25, 26)
• Muzibwereranso Kwa Anthu Achidwi (1 Akorinto 3:6)
• Muzithandiza Ophunzira Anu Kuti Akhale Olimba (Aheberi 6:1)
10:40 Achinyamata—Sankhani Njira Yomwe Ingakubweretsereni Mtendere (Mateyu 6:33; Luka 7:35; Yakobo 1:4)
11:00 Nyimbo Na. 135 ndi Zilengezo
11:10 VIDIYO: Mmene Abale Athu Akukhalira Mwamtendere Ngakhale Kuti . . .
• Akutsutsidwa
• Akudwala
• Akukumana ndi Mavuto a Zachuma
• Akukumana ndi Ngozi Zam’chilengedwe
11:45 NKHANI YA UBATIZO: Pitirizani Kuyenda “Panjira Yamtendere” (Luka 1:79; 2 Akorinto 4:16-18; 13:11)
12:15 Nyimbo Na. 54 ndi Kupuma
Masana
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 29
1:50 NKHANI YOSIYIRANA: Muzipewa Zinthu Zomwe Zingasokoneze Mtendere
• Kudzitama (Aefeso 4:22; 1 Akorinto 4:7)
• Nsanje (Afilipi 2:3, 4)
• Zachinyengo (Aefeso 4:25)
• Miseche (Miyambo 15:28)
• Mkwiyo (Yakobo 1:19)
2:45 VIDIYO YA NKHANI YA M’BAIBULO: Yehova Amatitsogolera Panjira Yamtendere—Mbali Yoyamba (Yesaya 48:17, 18)
3:15 Nyimbo Na. 130 ndi Zilengezo
3:25 NKHANI YOSIYIRANA: Muzifunafuna “Mtendere ndi Kuusunga” . . .
• Musamakwiye Msanga (Miyambo 19:11; Mlaliki 7:9; 1 Petulo 3:11)
• Muzipepesa (Mateyu 5:23, 24; Machitidwe 23:3-5)
• Muzikhululuka ndi Mtima Wonse (Akolose 3:13)
• Muzigwiritsa Ntchito Mwanzeru Mphatso ya Kulankhula (Miyambo 12:18; 18:21)
4:15 Muziteteza “Umodzi Wathu Pokhala Mwamtendere” (Aefeso 4:1-6)
4:50 Nyimbo Na. 113 ndi Pemphero Lomaliza