Anthu Okonda Mtendere
M’mawa
9:40 Kumvetsera Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 58 ndi Pemphero
10:00 Takulandirani Anthu Okonda Mtendere
10:15 Pitirizani Kufufuza Anthu Okonda Mtendere
10:30 Muzilola Kuti Kalonga Wamtendere Akuthandizeni Kufufuza Anthu Okonda Mtendere
10:55 Nyimbo Na. 103 ndi Zilengezo
11:05 Anthu Okonda Mtendere Saphunzira Nkhondo
11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:05 Nyimbo Na. 79
Masana
1:20 Kumvetsera Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 76
1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu
1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:15 Nkhani Yosiyirana: Anthu Okonda Mtendere Amathandizana
• “Muzifutukula Mtima Wanu”
• Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri
• Muzilemekeza Achikulire
3:00 Nyimbo Na. 57 ndi Zilengezo
3:10 Mmene Anthu Okonda Mtendere Amagonjetsera Choipa Pochita Chabwino
3:55 Nyimbo Na. 45 ndi Pemphero