Lowani mu Mpumulo wa Mulungu
M’mawa
9:40 Kumvetsera Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 87 ndi Pemphero
10:00 Kodi Tingalowe Bwanji mu Mpumulo wa Mulungu?
10:15 Kodi “Mawu a Mulungu Ndi Amoyo”—Mu Njira Yotani?
10:30 Pitirizani Kudalira Yehova Kuti Azikutsogolerani
10:55 Nyimbo Na. 89 ndi Zilengezo
11:05 Yehova Amadalitsa Anthu Omvera
11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:05 Nyimbo Na. 32
Masana
1:20 Kumvetsera Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 49
1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu
1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:15 Nkhani Yosiyirana: Amasangalatsa Mtima wa Yehova
• Achinyamata
• Alongo
• Achikulire
3:00 Nyimbo Na. 38 ndi Zilengezo
3:10 Muzitumikira Yehova Mosangalala
3:55 Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero