Muzisangalatsa Mtima wa Yehova!
M’MAWA
9:30 Kumvetsera Nyimbo
9:40 Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero
9:50 Muzisangalatsa Mtima wa Yehova!
10:05 Nkhani Yosiyirana: Muzitsanzira Makhalidwe 4 a Yehova
• Chilungamo
• Kugwiritsa Ntchito Mphamvu
• Nzeru
• Chikondi
11:05 Nyimbo Na. 81 ndi Zilengezo
11:15 Muzilemekeza Yehova Pamene ‘Mukubala Zipatso Zambiri’
11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:00 Nyimbo Na. 49
MASANA
1:10 Kumvetsera Nyimbo
1:20 Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero
1:30 Nkhani ya Baibulo ya Onse: Kodi Mungatani Kuti Muzisangalatsa Mulungu?
2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:30 Nyimbo Na. 35 ndi Zilengezo
2:40 Nkhani Yosiyirana: Muzisangalatsa Yehova . . .
• Pamoyo Wanu
• M’banja lanu
• Mumpingo Wanu
• M’dera Limene Mukukhala
3:40 ‘Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Chingakupatseni Mphamvu’
4:15 Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero