Banja la Yehova Logwirizana
M’mawa
9:30 Kumvetsera Nyimbo
9:40 Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero
9:50 Muziyamikira Mwayi Wanu Wokhala M’banja la Yehova
10:05 Nkhani Yosiyirana: Anathandiza Kuti Ena Azimva Bwino
• Elihu
• Lidiya
• Yesu
11:05 Nyimbo Na. 100 ndi Zilengezo
11:15 Pitirizani Kuthandiza Ena Kuti Akhale M’banja la Yehova
11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:00 Nyimbo Na. 135
Masana
1:10 Kumvetsera Nyimbo
1:20 Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero
1:30 Nkhani ya Baibulo ya Onse: Kodi Panyumba Panu Ndi Malo a Mpumulo Ndi Mtendere?
2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:30 Nyimbo Na. 136 ndi Zilengezo
2:40 Nkhani Yosiyirana: Muzilimbikitsa Mtendere
• Muzilankhula ‘Mawu Olimbikitsa’
• ‘Muziyenda M’chikondi’
• Muzipewa Adani Athu
3:40 ‘Tisamaleke Kuyamika Mulungu’ Chifukwa cha Abale ndi Alongo Athu
4:15 Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero