Khalani ndi ‘Chikhulupiriro’
M’MAWA
9:30 Kumvetsera Nyimbo
9:40 Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero
9:50 Mmene Tingasonyezere Kuti ‘Timakhulupirira’ Ndiponso Chifukwa Chake
10:05 Nkhani Yosiyirana: Muzitsanzira Anthu Amene Anasonyeza Chikhulupiriro
• Isaki ndi Rabeka
• Esitere
• Timoteyo
11:05 Nyimbo Na. 60 ndi Zilengezo
11:15 ‘Tili ndi Chikhulupiriro, Chotero Timalankhula’
11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:00 Nyimbo Na. 52
MASANA
1:10 Kumvetsera Nyimbo
1:20 Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero
1:30 Nkhani ya Baibulo ya Onse: Muzikhulupirira Mulungu “Amene Sanganame”
2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:30 Nyimbo Na. 54 ndi Zilengezo
2:40 Nkhani Yosiyirana: ‘Muziyenda mwa Chikhulupiriro’ Tsiku Lililonse
• “Musamade Nkhawa”
• “Muzigwiritsa Ntchito Bwino Nthawi Yanu”
• Musamakhale “Mbali ya Dziko”
3:40 “Yehova Amadziwa Anthu Ake”
4:15 Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero