Msonkhano Wadera wa Mboni za Yehova
Pulogalamu 2016-2017
Mutu: Yesetsani Kuti Muzikhulupirira Kwambiri Yehova—Aheb. 11:6.
M’mawa
9:30 Kumvetsera Nyimbo
9:40 Nyimbo Na. 12 ndi Pemphero
9:50 “Muzikhulupirira Mulungu” Nthawi Zonse
10:05 Yosiyirana: Mawu Oyerekezera Amene Amatithandiza Kukhulupirira Kwambiri Yehova
Chishango
Atate
Thanthwe
M’busa
11:05 Nyimbo Na. 22 ndi Zilengezo
11:15 “Limbitsani Chikhulupiriro Changa”
11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:00 Nyimbo Na. 7
Masana
1:10 Kumvetsera Nyimbo
1:20 Nyimbo Na. 54 ndi pemphero
1:30 Nkhani ya Onse: Kodi Chikhulupiriro Chenicheni N’chiyani Ndipo Tingachisonyeze Bwanji?
2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:30 Nyimbo Na. 30 ndi Zilengezo
2:40 Yosiyirana: Tayani “Tchimo Limene Limatikola Mosavuta”
Yehova Adzachotsa Zoipa Zonse
Yehova Adzakupatsani Zofunika pa Moyo
Yehova Adzaukitsa Akufa
3:40 Yehova Adzapereka Mphoto kwa Anthu a Chikhulupiriro Cholimba
4:15 Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero