Msonkhano Wadera wa Mboni za Yehova
Pulogalamu 2016-2017
Mutu: Musasiye Kukonda Yehova—Mat. 22:37.
M’mawa
9:40 Kumvetsera Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero
10:00 Tizikumbukira Lamulo Lalikulu Kwambiri
10:15 Tizikonda Mulungu Osati Dziko
10:30 Tiziphunzitsa Ena Kuti ‘Azikonda Dzina’ la Yehova”
10:55 Nyimbo Na. 112 ndi Zilengezo
11:05 “Munthu Amene Amakonda Mulungu Azikondanso M’bale Wake”
11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:05 Nyimbo Na. 34
Masana
1:20 Kumvetsera Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 73
1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu
1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:15 Makolo, Muziphunzitsa Ana Anu Kuti Azikonda Yehova
2:30 Achinyamata, Muzisonyeza Kuti Yehova ndi Mnzanu Wapamtima
2:45 Nyimbo Na. 106 ndi Zilengezo
2:55 Musasiye ‘Chikondi Chimene Munali Nacho Poyamba’
3:55 Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero