Pulogalamu ya Msonkhano Wadera ya 2016-2017—Wokhala ndi Woyang’anira Dera (CA-copgm17) Msonkhano Wadera wa Mboni za Yehova Yesetsani Kuti Muzikhulupirira Kwambiri Yehova—Aheb. 11:6 Muzimvetsera Mwachidwi Kuti Mupeze Mayankho a Mafunso Awa