Muzimvetsera Mwachidwi Kuti Mupeze Mayankho a Mafunso Awa:
N’chifukwa chiyani tiyenera kukhulupirira Mulungu nthawi zonse? (Maliko 11:22)
Kodi kuganizira mawu oyerekezera ofotokoza za Yehova kungatithandize bwanji? (Sal. 28:7; Luka 11:11-13; Deut. 32:4; Sal. 23:1)
Kodi tingalimbitse bwanji chikhulupiriro chathu? (Maliko 9:24)
Kodi “tchimo limene limatikola mosavuta” ndi liti, ndipo tingalipewe bwanji? (Aheb. 12:1)
N’chiyani chikutitsimikizira kuti anthu amene ali ndi chikhulupiriro cholimba adzalandira mphoto? (Aheb. 11:6)