“Chikondi Chimamangirira”
M’MAWA
9:30 Kumvetsera Nyimbo
9:40 Nyimbo Na. 90 ndi Pemphero
9:50 “Kudziwa Zinthu Kumachititsa Munthu Kudzitukumula, Koma Chikondi Chimamangirira”
10:05 Nkhani Yosiyirana: Ankalimbikitsa Ena
Baranaba
Paulo
Dorika
11:05 Nyimbo Na. 79 ndi Zilengezo
11:15 Muzichita Zambiri mu Utumiki Osati Kungolalikira Uthenga Wabwino
11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:00 Nyimbo Na. 52
MASANA
1:10 Kumvetsera Nyimbo
1:20 Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero
1:30 Nkhani ya Onse: Kodi Akhristu Achikondi Amalimbikitsa Bwanji Choonadi?
2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:30 Nyimbo Na. 101 ndi Zilengezo
2:40 Nkhani Yosiyirana: Muzithandiza Kuti Mpingo Wachikhristu Ukhale Wolimba
Muzikonda Choonadi
Muzisonyeza Kuti Malamulo a Mulungu Ndi Othandiza
Muzilimbikitsa Akhristu Anzanu
3:40 “Zonse Zimene Mukuchita, Muzichite Mwachikondi”
4:15 Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero