Kodi mungatani kuti banja lanu lizisangalala?
“Aliyense wa inu azikonda mkazi wake ngati mmene amadzikondera yekha komanso mkazi azilemekeza kwambiri mwamuna wake.”—Aefeso 5:33.
Baibulo limanena kuti
Anthu okwatirana azikhala okhulupirika m’banja.—Mateyu 19:4-6.
Ana amene amalemekeza komanso kumvera makolo awo, zinthu zimawayendera bwino.—Aefeso 6:1-3.
Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania