Kodi n’zotheka kukhala popanda zopweteka zilizonse?
Mulungu “adzapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo ndipo imfa sidzakhalaponso. Sipadzakhalanso kulira, kubuula kapena kupweteka.”—Chivumbulutso 21:4.
Baibulo limatitsimikizira kuti
Mulungu si amene amachititsa mavuto athu.—Yakobo 1:13.
Iye amamvetsa zimene timakumana nazo ndipo adzatipulumutsa ku mavuto athu onse.—Salimo 34:17-19.
Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania