Kodi okondedwa anu amene anamwalira mudzawaonanso?
“Nthawi ikubwera imene onse amene ali mʼmanda achikumbutso adzamva mawu ake ndipo adzatuluka.”—Yohane 5:28, 29.
Baibulo limatitsimikizira kuti
Mulungu adzaukitsa okondedwa athu amene anamwalira.—Machitidwe 24:15.
Iye akulakalaka kudzawaukitsa.—Yobu 14:13-15.
Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania