Mawu Oyamba
KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?
Kodi mukuona kuti mungapindule ndi mfundo yodziwika bwino iyi:
“Mulungu anakonda kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha”?—Yohane 3:16.
Magaziniyi ikufotokoza mmene mungapindulire ndi imfa ya Yesu.