Mawu Oyamba
KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?
Kodi mphatso yaikulu kwambiri imene Mulungu anatipatsa ndi iti?
Baibulo limati: “Mulungu anakonda kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha.”—Yohane 3:16.
Nsanja ya Olonda iyi ikufotokoza chifukwa chimene Mulungu anatumizira Yesu padziko lapansi kuti adzatifere komanso zimene tingachite posonyeza kuti timayamikira mphatsoyi.