Mawu Oyamba
KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?
Kodi mawu awa adzakwaniritsidwadi?
“Mulungu . . . adzapukuta misozi yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.”—Chivumbulutso 21:3, 4.
Magaziniyi ikufotokoza mmene Mulungu adzakwaniritsire lonjezo limeneli komanso phindu limene mudzapeze mawuwa akadzakwaniritsidwa.