Mawu Oyamba
KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?
Kodi mungayankhe bwanji munthu wina atakufunsani kuti kumwamba n’kotani?
Yesu angatithandize kudziwa za kumwamba chifukwa anati: “Ine ndine wochokera kumwamba.”—Yohane 8:23.
Nsanja ya Olonda iyi ikufotokoza zimene Yesu ndiponso Atate ake ananena zokhudza kumwamba.