Mawu Oyamba
KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?
Kodi chinali cholinga cha Mulungu kuti anthufe tizifa? Baibulo limati: “[Mulungu] adzapukuta misozi yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.”—Chivumbulutso 21:4.
Magaziniyi ikufotokoza zimene Baibulo limanena pa nkhani ya imfa.