Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp18 No. 1 tsamba 16
  • Kodi inuyo mukuganiza bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi inuyo mukuganiza bwanji?
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)——2018
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Baibulo lingakuthandizeni kuti Mulungu akhale mnzanu?
  • Mulungu Akukuitanani Kuti Mukhale Bwenzi Lake
    Mungathe Kukhala Bwenzi la Mulungu!
  • Yehova Akhoza Kukhala Mnzanu
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yokhala Ndi Anzathu?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Kodi Mungatani Kuti Mukhale Bwenzi Labwino?
    Galamukani!—2014
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)——2018
wp18 No. 1 tsamba 16
Mwamuna ndi mkazi wake akuwerenga Baibulo

Kodi Inuyo Mukuganiza Bwanji?

Kodi Baibulo lingakuthandizeni kuti Mulungu akhale mnzanu?

ANTHU ENA AMAKHULUPIRIRA . . .

kuti sangakhale mabwenzi a Mulungu chifukwa amaona kuti ndi ochimwa. Ena amaganiza kuti Mulungu satidera nkhawa. Kodi inuyo mukuganiza bwanji?

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Mulungu “amakonda anthu owongoka mtima.” (Miyambo 3:32) Tikamamvera Mulungu, tingathe kukhala mabwenzi ake.

MFUNDO ZINANSO ZOMWE TIKUPHUNZIRA M’BAIBULO

  • Mulungu amafuna kuti tikhale anzake.​—Yakobo 4:8.

  • Popeza Yehova ndi Mnzathu, amakhala wokonzeka kutithandiza komanso kutikhululukira.​—Salimo 86:5.

  • Mabwenzi a Mulungu amakonda zimene iye amakonda ndiponso amadana ndi zimene iye amadana nazo.​—Aroma 12:9.

Kuti mudziwe zambiri zokhudza zimene mungachite kuti muzisangalatsa Mulungu, werengani mutu 12 m’buku ili, Zimene Baibulo Limaphunzitsa lofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova. Bukuli likupezekanso pawebusaiti yathu ya jw.org/ny

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena