Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp19 No. 3 tsamba 16
  • Kodi Anthu Amene Anamwalira Adzakhalanso Ndi Moyo?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Anthu Amene Anamwalira Adzakhalanso Ndi Moyo?
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • TAONANI ZIMENE BAIBULO LIMANENA:
  • Chiyembekezo cha Chiukiriro N’chotsimikizirika!
    Nsanja ya Olonda—2000
  • Mabiliyoni Amene Ali Akufa Tsopano Adzakhala’nso ndi Moyo Posachedwa
    Kodi Moyo Uno Ndiwo Wokha Umene Ulipo?
  • Kudzakhala Kuuka kwa Olungama
    Nsanja ya Olonda—1995
  • Achibale Anu Ndi Anzanu Amene Anamwalira Adzakhalanso Ndi Moyo
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
wp19 No. 3 tsamba 16

Kodi Anthu Amene Anamwalira Adzakhalanso Ndi Moyo?

Mmodzi mwa asayansi amene atchulidwa poyamba paja, wanyamula chithunzi cha banja la anthu achikulire omwe atchulidwa munkhani yoyamba

Imfa imakhudza aliyense. Koma kodi imfa ndi mathero a zonse? Kodi anthu amene anamwalira ndiye kuti basi anaiwalidwa? Kodi pali chiyembekezo chilichonse chokhudza anthu amene anamwalira?

TAONANI ZIMENE BAIBULO LIMANENA:

ANTHU AMENE ANAMWALIRA SANAIWALIDWE

“Onse ali m’manda achikumbutso . . . adzatuluka.”—Yohane 5:28, 29.

Mulungu sanaiwale anthu amene anamwalira ndipo adzaukitsa onse amene ali m’manda achikumbutso.

AKUFA ADZAUKITSIDWA PADZIKOLI

“Kudzakhala kuuka kwa olungama ndi osalungama omwe.”​—Machitidwe 24:15.

Anthu mamiliyoni ambirimbiri adzaukitsidwa n’kupatsidwa mwayi wokhala ndi moyo kwamuyaya m’dziko la mtendere.

CHIYEMBEKEZO CHOTI AKUFA ADZAUKITSIDWA N’CHODALIRIKA

“[Mulungu] amawerenga nyenyezi zonse, ndipo zonsezo amazitchula mayina ake.”​—Salimo 147:4.

Ngati Mulungu amakwanitsa kutchula nyenyezi iliyonse dzina, ndiye kuti akukumbukira anthu amene akufuna kudzawaukitsa.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena